Eksodo 26:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo uzipanga zokowera makumi asanu zamkuwa, ndi kukowetsa zokowerazo m'magangomo, ndi kumanga pamodzi hemalo likhale limodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo uzipanga zokowera makumi asanu zamkuwa, ndi kukowetsa zokowerazo m'magangomo, ndi kumanga pamodzi hemalo likhale limodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 “Upange zomangira makumi asanu zamkuŵa, ndipo uziike m'magongamo. Choncho uphatikize pamodzi nsalu ziŵirizo, kuti pakhale chihema chimodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Kenaka upange ngowe 50 zamkuwa ndipo uzilowetse mu zokolowekazo. Ndiye uphatikize nsalu ziwirizo kuti tentiyo ikhale imodzi. Onani mutuwo |