Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 26:11 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Kenaka upange ngowe 50 zamkuwa ndipo uzilowetse mu zokolowekazo. Ndiye uphatikize nsalu ziwirizo kuti tentiyo ikhale imodzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

11 Ndipo uzipanga zokowera makumi asanu zamkuwa, ndi kukowetsa zokowerazo m'magangomo, ndi kumanga pamodzi hemalo likhale limodzi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo uzipanga zokowera makumi asanu zamkuwa, ndi kukowetsa zokowerazo m'magangomo, ndi kumanga pamodzi hemalo likhale limodzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 “Upange zomangira makumi asanu zamkuŵa, ndipo uziike m'magongamo. Choncho uphatikize pamodzi nsalu ziŵirizo, kuti pakhale chihema chimodzi.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 26:11
4 Mawu Ofanana  

Upange zokolowekamo 50 mʼmphepete mwa nsalu imodzi yotsirizira ya nsalu yoyamba yolumikiza ija. Upangenso zokolowekamo zina 50 mʼmphepete mwa nsalu yotsirizira ya nsalu inanso yolumikiza ija.


Theka lotsalira la nsaluyo lidzalendewera kumbuyo kwa chihemacho.


Ulumikize nsalu zisanu kuti ikhale nsalu imodzi. Uchite chimodzimodzi ndi nsalu zisanu zinazo.


Kenaka upange ngowe zagolide makumi asanu zolumikizira nsalu ziwirizo kuti zipange chihema chimodzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa