Eksodo 25:36 - Buku Lopatulika36 Mitu yao ndi mphanda zao zikhale zotuluka m'mwemo; chonsechi chikhale chosulika chimodzi cha golide woona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Mitu yao ndi mphanda zao zikhale zotuluka m'mwemo; chonsechi chikhale chosulika chimodzi cha golide woona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Nkhunjezo pamodzi ndi mphandazo zidzapangidwire kumodzi ndi choikaponyalecho. Chonsecho chidzangokhala chimodzi, chopangidwa ndi golide, chosula ndi nyundo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Mphukira ndi nthambi zonse zisulidwe kumodzi ndi choyikapo nyalecho ndi golide wabwino kwambiri. Onani mutuwo |