Eksodo 24:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Mose ndi Aroni, Nadabu ndi Abihu, ndi akulu a Israele makumi asanu ndi awiri anakwerako; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Mose ndi Aroni, Nadabu ndi Abihu, ndi akulu a Israele makumi asanu ndi awiri anakwerako; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Tsono Mose, Aroni, Nadabu ndi Abihu ndiponso anthu 70 mwa atsogoleri aja a Aisraele, adakwera phiri, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Kenaka Mose pamodzi ndi Aaroni, Nadabu, Abihu ndi akuluakulu makumi asanu ndi awiri a Israeli aja anakwera ku phiri, Onani mutuwo |