Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 24:15 - Buku Lopatulika

15 Ndipo Mose anakwera m'phirimo, ndi mtambo unaphimba phirilo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Ndipo Mose anakwera m'phirimo, ndi mtambo unaphimba phirilo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Tsono Mose adakwera phiri, ndipo phirilo lidaphimbidwa ndi mtambo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Mose atakwera ku phiri kuja mtambo unaphimba phirilo.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 24:15
6 Mawu Ofanana  

Pamenepo Solomoni anati, Yehova anati kuti adzakhala mu mdima wandiweyani.


Ndipo kunali tsiku lachitatu, m'mawa, panali mabingu ndi zimphezi, ndi mtambo wakuda bii paphiripo, ndi liu la lipenga lolimbatu; ndi anthu onse okhala kutsasa ananjenjemera.


Ndipo Yehova anatsikira paphiri la Sinai, pamutu pake paphiri; ndipo Yehova anaitana Mose akwere pamutu paphiri; ndi Mose anakwerapo.


Ndipo Yehova anati kwa Mose, Taona, ndikudza kwa iwe mu mtambo wakuda bii, kuti anthu amve pamene ndilankhula ndi iwe, ndi kuti akuvomereze nthawi zonse. Pakuti Mose adauza Yehova mau a anthuwo.


Ndipo ulemerero wa Yehova unakhalabe paphiri la Sinai, ndi mtambo unaliphimba masiku asanu ndi limodzi; ndipo tsiku lachisanu ndi chiwiri Iye ali m'kati mwa mtambo anaitana Mose.


Akali chilankhulire, onani, mtambo wowala unawaphimba iwo: ndipo onani, mau ali kunena mumtambo, Uyu ndiye Mwana wanga wokondedwa, mwa iyeyu ndikondwera, mverani Iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa