Eksodo 24:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo anauka Mose, ndi Yoswa mtumiki wake; ndipo Mose anakwera m'phiri la Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo anauka Mose, ndi Yoswa mtumiki wake; ndipo Mose anakwera m'phiri la Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Apo Mose adanyamuka pamodzi ndi mtumiki wake Yoswa, ndipo Moseyo adakwera phiri la Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ndipo anayamba ulendo wopita ku phiri la Mulungu pamodzi ndi womuthandiza wake Yoswa. Onani mutuwo |