Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 23:28 - Buku Lopatulika

28 Ndipo ndidzatumiza mavu akutsogolere amene adzaingitsa Ahivi, Akanani, ndi Ahiti, pamaso pako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 Ndipo ndidzatumiza mavu akutsogolere amene adzaingitsa Ahivi, Akanani, ndi Ahiti, pamaso pako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 Ndidzapirikitsa Ahivi, Akanani ndi Ahiti, inu musanafike, ndipo adzathaŵa monga ngati ndaŵatumira mavu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Ahivi, Akanaani ndi Ahiti adzathawa ngati kuti ndawatumizira mavu.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 23:28
7 Mawu Ofanana  

Akeni ndi Akenizi, Akadimoni,


Mudasoseratu pookapo, idagwiritsa mizu yake, ndipo unadzaza dziko.


ndipo ndidzatuma mthenga akutsogolere; ndipo ndidzapirikitsa Akanani, ndi Aamori, ndi Ahiti, ndi Aperizi, Ahivi, ndi Ayebusi;


Dzisungire chimene Ine ndikuuza lero lino: taona, ndiingitsa pamaso pako Aamori ndi Akanani, ndi Ahiti ndi Aperizi, ndi Ahivi, ndi Ayebusi.


Mulungu wamuyaya ndiye mokhaliramo mwako; ndi pansipo pali manja osatha. Ndipo aingitsa mdani pamaso pako, nati, Ononga.


Komanso Yehova Mulungu wanu adzatumiza mavu pakati pao, kufikira ataonongeka otsalawo, ndi akubisala pamaso panu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa