Eksodo 23:26 - Buku Lopatulika26 M'dziko mwanu simudzakhala wakutaya mwana, kapena wosabala; ndidzakwaniritsa kuwerenga kwa masiku ako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 M'dziko mwanu simudzakhala wakutaya mwana, kapena wosabala; ndidzakwaniritsa kuwerenga kwa masiku ako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Palibe mkazi amene adzapititse padera m'dziko mwanumo, ndipo wosabala sadzaoneka. Ndidzakupatsani moyo wautali. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Palibe mkazi amene adzapite padera kapena kukhala wosabereka mʼdziko mwanu. Ndidzakupatsani moyo wautali. Onani mutuwo |