Eksodo 22:20 - Buku Lopatulika20 Wakuphera nsembe mulungu wina, wosati Yehova yekha, aonongeke konse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Wakuphera nsembe mulungu wina, wosati Yehova yekha, aonongeke konse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 “Aliyense wopereka nsembe kwa milungu, osati kwa Chauta yekha, aphedwe ameneyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 “Aliyense wopereka nsembe kwa mulungu wina osati Yehova awonongedwe. Onani mutuwo |