Eksodo 22:18 - Buku Lopatulika18 Wanyanga usamlola akhale ndi moyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Wanyanga usamlola akhale ndi moyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 “Munthu wamkazi wochita zaufiti, musamlole kuti akhale moyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 “Musayilole mfiti yayikazi kuti ikhale ndi moyo. Onani mutuwo |