Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 21:7 - Buku Lopatulika

7 Ndipo munthu akagulitsa mwana wake wamkazi akhale mdzakazi, iyeyu asatuluke monga amatuluka anyamata.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndipo munthu akagulitsa mwana wake wamkazi akhale mdzakazi, iyeyu asatuluke monga amatuluka anyamata.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 “Munthu akagulitsa mwana wake wamkazi ku ukapolo, mwanayo sadzaomboledwa monga m'mene amachitira ndi akapolo aamuna.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 “Ngati munthu agulitsa mwana wake wamkazi kukhala mdzakazi, mwanayo asamasulidwe monga achitira ndi akapolo aamuna.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 21:7
4 Mawu Ofanana  

Koma tsopano thupi lathu likunga thupi la abale athu, ana athu akunga ana ao; ndipo taonani, titengetsa ana athu aamuna ndi aakazi akhale akapolo, ndi ana athu aakazi ena tawatengetsa kale; ndipo tilibe ife mphamvu ya kuchitapo kanthu; ndi minda yathu, ndi minda yathu yampesa, nja ena.


pamenepo mbuye wake azifika naye kwa oweruza, nafike naye kukhomo, kapena kumphuthu, ndipo mbuye wake am'boole khutu lake ndi lisungulo; ndipo iye azimgwirira ntchito masiku onse.


Akapanda kumkonda mbuye wake, amene anamtoma mwini yekha, azilola kuti amuombole; alibe mphamvu yakumgulitsa kwa anthu achilendo, popeza wachita naye monyenga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa