Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 21:31 - Buku Lopatulika

31 Ingakhale yatunga mwana wamwamuna kapena wamkazi, aichitire monga mwa chiweruzo ichi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

31 Ingakhale yatunga mwana wamwamuna kapena wamkazi, aichitire monga mwa chiweruzo ichi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

31 Ng'ombe ikapha mnyamata kapena mtsikana, lamulo lake ndi lomwelo ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

31 Lamulo ili ligwirenso ntchito ngati ngʼombeyo yagunda mwana wamwamuna kapena wamkazi.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 21:31
4 Mawu Ofanana  

Ng'ombe ikatunga mwamuna kapena mkazi, nafa, aiponyetu miyala ng'ombeyo, osadya nyama yake; koma mwini ng'ombeyo azimasuka.


Akamuikira dipo, azipereka chiombolo cha moyo wake monga mwa zonse adamuikira.


Ng'ombeyo ikatunga mnyamata kapena mdzakazi, azipatsa mbuye wake ndalama za masekeli a siliva makumi atatu, ndipo ng'ombeyo aiponye miyala.


Anaimirira, nandengulitsa dziko lapansi; anapenya, nanjenjemeretsa amitundu; ndi mapiri achikhalire anamwazika, zitunda za kale lomwe zinawerama; mayendedwe ake ndiwo a kale lomwe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa