Eksodo 21:23 - Buku Lopatulika23 Koma ngati kupweteka kukalipo, uzipereka moyo kulipa moyo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Koma ngati kuphweteka kukalipo, uzipereka moyo kulipa moyo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Koma maiyo akampweteka, chilango chake chidzakhala chotere: moyo kulipa moyo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Koma ngati wavulazidwa kwambiri, ndiye malipiro ake adzakhala motere: moyo kulipa moyo, Onani mutuwo |