Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 19:25 - Buku Lopatulika

25 Pamenepo Mose anawatsikira anthu, nanena nao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Pamenepo Mose anawatsikira anthu, nanena nao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Apo Mose adatsikira kwa anthu kuja kukaŵauza zimenezo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Ndipo Mose anatsika ndi kukawawuza anthuwo.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 19:25
3 Mawu Ofanana  

Ndipo Yehova anati kwa iye, Muka, tsika; nukwere iwe ndi Aroni pamodzi ndi iwe; koma ansembe ndi anthu asapyole kukwera kwa Yehova, angawapasule.


Ndipo Mulungu ananena mau onse amenewa, nati,


(ndinalinkuima pakati pa Yehova ndi inu muja, kukulalikirani mau a Yehova; popeza munachita mantha chifukwa cha moto, osakwera m'phirimo) ndi kuti:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa