Eksodo 19:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo Mose anatulutsa anthu kutsasa, kuti akomane ndi Mulungu; ndipo anaima patsinde paphiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo Mose anatulutsa anthu kutsasa, kuti akomane ndi Mulungu; ndipo anaima patsinde pa phiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Mose adaŵatsogolera anthuwo kuchoka kumahemako, kuti akakumane ndi Mulungu, ndipo onsewo adaima patsinde pa phiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Ndipo Mose anatsogolera anthu kutuluka mʼmisasa kukakumana ndi Mulungu, ndipo anayima mʼmunsi mwa phiri. Onani mutuwo |