Eksodo 19:11 - Buku Lopatulika11 Nakonzekeretu tsiku lachitatu; pakuti tsiku lachitatu Yehova adzatsika paphiri la Sinai pamaso pa anthu onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Nakonzekeretu tsiku lachitatu; pakuti tsiku lachitatu Yehova adzatsika pa phiri la Sinai pamaso pa anthu onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 ndipo akhale okonzeka mkucha. Pa tsiku limenelo, Ine Chauta ndidzatsika pa phiri la Sinai, ndipo kumeneko anthu onse adzandiwona Ine. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 ndipo akhale atakonzeka pofika tsiku lachitatu, chifukwa tsiku limenelo Yehova adzatsika pa phiri la Sinai anthu onse akuona. Onani mutuwo |