Eksodo 18:18 - Buku Lopatulika18 Udzalema konse, iwe ndi anthu amene uli nao; pakuti chikukanika chinthu ichi; sungathe kuchichita pa wekha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Udzalema konse, iwe ndi anthu amene uli nao; pakuti chikukanika chinthu ichi; sungathe kuchichita pa wekha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Inu mudzafooka msanga, pamodzi ndi anthu muli nawoŵa. Ntchito imeneyi njaikulu kuposa mphamvu zanu, ndipo simungaithe nokha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ntchitoyi ndi yayikulu kuposa mphamvu zanu. Inu simungathe kuyigwira nokha. Inu pamodzi ndi anthuwa amene amabwera kwa inu mudzatopa. Onani mutuwo |