Eksodo 18:17 - Buku Lopatulika17 Koma mpongozi wa Mose ananena naye, Chinthu uchitachi sichili chabwino ai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Koma mpongozi wa Mose ananena naye, Chinthu uchitachi sichili chabwino ai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Apo Yetero mpongozi wa Moseyo adati, “Simukuchita bwino ai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Mpongozi wa Mose anayankha kuti, “Zimene mukuchitazi si zabwino. Onani mutuwo |