Eksodo 16:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo kudzakhala tsiku lachisanu ndi chimodzi, kuti azikonza umene adabwera nao, ataonjezapo muyeso unzake wa pa tsiku limodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo kudzakhala tsiku lachisanu ndi chimodzi, kuti azikonza umene adabwera nao, ataonjezapo muyeso unzake wa pa tsiku limodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Pa tsiku lachisanu ndi chimodzi, pokonza chimene adatola adzapeza kuti nchokwanira masiku aŵiri.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Pa tsiku lachisanu ndi chimodzi, pamene azidzakonza buledi amene abwera naye, adzapeza kuti ndi wokwanira masiku awiri.” Onani mutuwo |