Eksodo 16:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo anauola m'mawa ndi m'mawa, yense monga mwa njala yake; popeza likatentha dzuwa umasungunuka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo anauola m'mawa ndi m'mawa, yense monga mwa njala yake; popeza likatentha dzuwa umasungunuka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Ankatola m'maŵa mulimonse, ndipo aliyense ankatola monga m'mene ankasoŵera. Koma dzuŵa likatentha, tinthuto tinkasungunuka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Mmawa uliwonse aliyense amatola zimene amazifuna, ndipo dzuwa likatentha zimasungunuka. Onani mutuwo |