Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 16:2 - Buku Lopatulika

2 Ndipo khamu lonse la ana a Israele linadandaulira Mose ndi Aroni m'chipululu;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndipo khamu lonse la ana a Israele linadandaulira Mose ndi Aroni m'chipululu

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Ndipo khamu lonse lidadandaulira Mose ndi Aroni m'chipululu muja kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Mʼchipululumo gulu lonse linadandaulira Mose ndi Aaroni

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 16:2
10 Mawu Ofanana  

Koma asanagone, anthu a m'mzindamo anthu a Sodomu, anazinga nyumba, anyamata ndi okalamba, anthu onse a m'mbali zonse;


Koma anaiwala ntchito zake msanga; sanalindire uphungu wake:


koma anadandaula m'mahema mwao, osamvera mau a Yehova.


Makolo athu sanadziwitse zodabwitsa zanu mu Ejipito; sanakumbukire zachifundo zanu zaunyinji; koma anapikisana ndi Inu kunyanja, ku Nyanja Yofiira.


Ndipo anati kwa Mose, Kodi mwatichotsera kuti tikafe m'chipululu chifukwa panalibe manda mu Ejipito? Nchiyani ichi mwatichitira kuti mwatitulutsa mu Ejipito?


Ndipo anthu anadandaulira Mose, ndi kuti, Tidzamwa chiyani?


Ndipo pomwepo anthu anamva ludzu lokhumba madzi; ndi anthu anadandaulira Mose, nati, Munatikwezeranji kuchokera ku Ejipito, kudzatipha ife ndi ana athu ndi zoweta zathu ndi ludzu?


ndipo ananena nao, Yehova akupenyeni, naweruze; pakuti mwatinyansitsa pamaso pa Farao, ndi pamaso pa anyamata ake, ndi kuwapatsa lupanga m'dzanja lao kutipha nalo.


popeza anthu onse awa amene adaona ulemerero wanga, ndi zizindikiro zanga, ndidazichita mu Ejipito ndi m'chipululu, koma anandiyesa Ine kakhumi aka, osamvera mau anga;


Kapena musadandaula, monga ena a iwo anadandaula, naonongeka ndi woonongayo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa