Eksodo 15:23 - Buku Lopatulika23 Pamene anafika ku Mara sanakhoze kumwa madzi a pa Mara, pakuti anali owawa; chifukwa chake anatcha dzina lake Mara. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Pamene anafika ku Mara sanakhoze kumwa madzi a Mara, pakuti anali owawa; chifukwa chake anatcha dzina lake Mara. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Ndipo adakafika ku Mara, koma kumeneko madzi ake anali oŵaŵa, kotero kuti sadathe kuŵamwa. Nchifukwa chake malowo adaŵatcha kuti Mara. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Ndipo anafika ku Mara. Koma sanathe kumwa madzi akumeneko chifukwa anali owawa. (Ndi chifukwa chake malowo amatchedwa Mara). Onani mutuwo |