Eksodo 14:29 - Buku Lopatulika29 Koma ana a Israele anayenda pouma pakati pa nyanja; ndi madziwo anakhala ngati khoma kwa iwo, palamanja ndi lamanzere. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Koma ana a Israele anayenda pouma pakati pa nyanja; ndi madziwo anakhala ngati khoma kwa iwo, palamanja ndi lamanzere. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Koma Aisraele onse aja adaoloka nyanjayo pansi pali pouma, madzi atangoima pa mbali zonse ziŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Koma Aisraeli aja anawoloka nyanja pansi pali powuma, madzi atachita khoma kumanja ndi kumanzere kwawo. Onani mutuwo |