Eksodo 14:28 - Buku Lopatulika28 Popeza madziwo anabwerera, namiza magaleta ndi apakavalo, ndiwo nkhondo yonse ya Farao imene idalowa pambuyo pao m'nyanja; sanatsale wa iwowa ndi mmodzi yense. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Popeza madziwo anabwerera, namiza magaleta ndi apakavalo, ndiwo nkhondo yonse ya Farao imene idalowa pambuyo pao m'nyanja; sanatsale wa iwowa ndi mmodzi yense. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Ndipo madziwo adabwerera, namiza magaleta aja ndi oŵayendetsawo, pamodzi ndi gulu lonse lankhondo la Farao lija linkaŵatsatali. Palibe ndi mmodzi yemwe amene adapulumuka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Madzi anabwerera ndi kumiza magaleta ndi okwera akavalo, asilikali ankhondo onse amene anatsatira Aisraeli mʼnyanja, palibe ndi mmodzi yemwe amene anapulumuka. Onani mutuwo |