Eksodo 14:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo ana a Israele analowa pakati pa nyanja pouma; ndi madziwo anakhala kwa iwo ngati khoma palamanja, ndi palamanzere. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo ana a Israele analowa pakati pa nyanja pouma; ndi madziwo anakhala kwa iwo ngati khoma palamanja, ndi palamanzere. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 ndipo adakhala ngati chipupa pa mbali zonse ziŵiri, motero Aisraele adaoloka pouma. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Ndipo Aisraeli anawoloka pakati pa nyanja powuma, madzi atasanduka khoma kumanja ndi kumanzere kwawo. Onani mutuwo |