Eksodo 14:12 - Buku Lopatulika12 Si awa mauwo tinalankhula nanu mu Ejipito ndi kuti, Tilekeni, kuti tigwirire ntchito Aejipito? Pakuti kutumikira Aejipito kutikomera si kufa m'chipululu ai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Si awa mauwo tinalankhula nanu m'Ejipito ndi kuti, Tilekeni, kuti tigwirire ntchito Aejipito? Pakuti kutumikira Aejipito kutikomera si kufa m'chipululu ai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Kodi ife tisanachoke ku Ejipito, sitidakuuzirenitu zimenezi? Ife tidaanena kuti, ‘Mutileke, tikhalebe akapolo a Aejipito.’ Zidakatikomera ife kukhalabe akapolo kupambana kuti tifere kuchipululu kuno.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Kodi sindizo zimene tinakuwuza mʼdziko la Igupto? Ife tinati, ‘Tileke titumikire Aigupto?’ Zikanatikomera kutumikira Aigupto kulekana ndi kufa mʼchipululu muno.” Onani mutuwo |