Eksodo 14:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo anati kwa Mose, Kodi mwatichotsera kuti tikafe m'chipululu chifukwa panalibe manda mu Ejipito? Nchiyani ichi mwatichitira kuti mwatitulutsa mu Ejipito? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo anati kwa Mose, Kodi mwatichotsera kuti tikafe m'chipululu chifukwa panalibe manda m'Ejipito? Nchiyani ichi mwatichitira kuti mwatitulutsa m'Ejipito? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Adafunsa Mose kuti, “Kodi nchifukwa chakuti ku Ejipito kunalibe malo a manda, kuti inuyo mutifikitse kuchipululu kuno kuti tidzafe? Mwatichita chiyani potitulutsa ku Ejipito? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Iwo anafunsa Mose kuti, “Kodi nʼchifukwa chakuti kunalibe manda ku dziko la Igupto kuti iwe utibweretse muno mʼchipululu kuti tidzafe? Chimene watichitachi nʼchiyani, kutitulutsa mʼdziko la Igupto? Onani mutuwo |