Eksodo 13:22 - Buku Lopatulika22 sanachotse mtambo usana, kapena mtambo wamoto usiku, pamaso pa anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 sanachotse mtambo usana, kapena mtambo wamoto usiku, pamaso pa anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Nthaŵi zonse chipilala chamtambo chinkatsogolera anthu masana, ndipo chipilala chamoto chinkaŵatsogolera usiku. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Usana, chipilala cha mtambo ndi usiku, chipilala cha moto zinali patsogolo kuwatsogolera anthu aja. Onani mutuwo |