Eksodo 13:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo anachokera ku Sukoti, nagona ku Etamu, pa malekezero a chipululu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo anachokera ku Sukoti, nagona ku Etamu, pa malekezero a chipululu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Aisraele adachoka ku Sukoti, nakagona ku Etamu m'mbali mwa chipululu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Atachoka ku Sukoti anakagona ku Etamu mʼmphepete mwa chipululu. Onani mutuwo |