Eksodo 12:51 - Buku Lopatulika51 Ndipo kunakhala tsiku lomwelo, kuti Yehova anatulutsa ana a Israele m'dziko la Ejipito, monga mwa makamu ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201451 Ndipo kunakhala tsiku lomwelo, kuti Yehova anatulutsa ana a Israele m'dziko la Ejipito, monga mwa makamu ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa51 Pa tsiku lomwelo ndi pamene Chauta adatulutsa Aisraele ku Ejipito mwa magulumagulu ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero51 Ndipo tsiku lomwelo Yehova anatulutsa gulu lonse la ana a Israeli mʼdziko la Igupto.” Onani mutuwo |