Eksodo 12:35 - Buku Lopatulika35 Ndipo ana a Israele anachita monga mwa mau a Mose; napempha Aejipito zokometsera zasiliva, ndi zagolide, ndi zovala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Ndipo ana a Israele anachita monga mwa mau a Mose; napempha Aejipito zokometsera zasiliva, ndi zagolide, ndi zovala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Ndiponso Aisraele anali atachita monga momwe Mose adaaŵauzira. Adaapempha kwa Aejipitowo zodzikongoletsera zasiliva ndi zagolide, ndiponso zovala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Aisraeli anachita monga anawawuzira Mose kuti apemphe kwa Aigupto zozikongoletsera zasiliva ndi zagolide ndi zovala. Onani mutuwo |