Eksodo 10:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo Farao ananena naye, Choka pano, uzichenjera usaonenso nkhope yanga; pakuti tsiku limene uonanso nkhope yanga udzafa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo Farao ananena naye, Choka pano, uzichenjera usaonenso nkhope yanga; pakuti tsiku limene uonanso nkhope yanga udzafa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Farao adauza Mose kuti, “Choka apa. Chenjera, ndipo usafikenso pamaso panga, chifukwa tsiku lomwe ndidzakuwonelo, udzaphedwa ndithu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Farao anati kwa Mose, “Choka pamaso panga! Uwonetsetse kuti usadzaonekerenso pamaso panga! Tsiku limene ndidzakuonenso udzafa.” Onani mutuwo |