Eksodo 1:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo mfumu ya Aejipito inaitana anamwino, ninena nao, Mwachita ichi chifukwa ninji, ndi kuleka ana aamunawo akhale ndi moyo? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo mfumu ya Aejipito inaitana anamwino, ninena nao, Mwachita ichi chifukwa ninji, ndi kuleka ana amunawo akhale ndi moyo? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Tsono mfumu ija idaŵaitana azamba aja niŵafunsa kuti, “Chifukwa chiyani mwaŵaleka ana aamuna osaŵapha?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Kenaka mfumu ya Igupto inayitanitsa azamba aja ndi kuwafunsa kuti, “Chifukwa chiyani mwachita zimenezi? Bwanji mwasiya ana aamuna kuti akhale ndi moyo?” Onani mutuwo |