Danieli 9:8 - Buku Lopatulika8 Yehova, kwa ife kuli manyazi a nkhope yathu, kwa mafumu athu, kwa akalonga athu, ndi kwa makolo athu; pakuti takuchimwirani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ambuye, kwa ife kuli manyazi a nkhope yathu, kwa mafumu athu, kwa akalonga athu, ndi kwa makolo athu; pakuti takuchimwirani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Inu Yehova, ife ndi mafumu athu, akalonga athu ndi makolo athu tili ndi manyazi chifukwa takuchimwirani. Onani mutuwo |