Danieli 9:10 - Buku Lopatulika10 sitinamvere mau a Yehova Mulungu wathu, kuyenda m'malamulo ake anatiikirawo pamaso pathu, mwa atumiki ake aneneri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 sitinamvera mau a Yehova Mulungu wathu, kuyenda m'malamulo ake anatiikirawo pamaso pathu, mwa atumiki ake aneneri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ife sitinamvere Yehova Mulungu wathu kapena kusunga malamulo ake amene anatipatsa kudzera mwa aneneri atumiki ake. Onani mutuwo |