Danieli 8:14 - Buku Lopatulika14 Nati kwa ine, Mpaka masiku zikwi ziwiri mphambu mazana atatu usana ndi usiku; pamenepo malo opatulika adzayesedwa olungama. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Nati kwa ine, Mpaka masiku zikwi ziwiri mphambu mazana atatu usana ndi usiku; pamenepo malo opatulika adzayesedwa olungama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Iye anandiyankha kuti, “Zidzachitika patapita masiku 2,300; pambuyo pake malo opatulika adzabwezeretsedwa monga kale.” Onani mutuwo |