Danieli 7:17 - Buku Lopatulika17 Zilombo zazikulu izi zinai ndizo mafumu anai amene adzauka padziko lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Zilombo zazikulu izi zinai ndizo mafumu anai amene adzauka pa dziko lapansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 ‘Zirombo zikuluzikulu zinayi zija ndi maufumu anayi amene adzaoneka pa dziko lapansi. Onani mutuwo |