Danieli 6:1 - Buku Lopatulika1 Kudamkomera Dariusi kuikira ufumuwo akalonga zana limodzi mphambu makumi awiri akhale m'madera onse a ufumu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Kudamkomera Dariusi kuikira ufumuwo akalonga zana limodzi mphambu makumi awiri akhale m'madera onse a ufumu; Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Kunamukomera Dariyo kusankha akalonga 120 kuti alamulire mu ufumu wonse, Onani mutuwo |