Danieli 5:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo Dariusi Mmedi analandira ufumuwo ali wa zaka makumi asanu ndi limodzi mphambu ziwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo Dariusi Mmedi analandira ufumuwo ali wa zaka makumi asanu ndi limodzi mphambu ziwiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 ndipo Dariyo Mmedi analanda ufumuwo ali ndi zaka 62. Onani mutuwo |