Danieli 5:8 - Buku Lopatulika8 Pamenepo analowa anzeru onse a mfumu, koma sanakhoze kuwerenga lembalo, kapena kudziwitsa mfumu kumasulira kwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Pamenepo analowa anzeru onse a mfumu, koma sanakhoze kuwerenga lembalo, kapena kudziwitsa mfumu kumasulira kwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Pamenepo anzeru onse a mfumu anabwera, koma sanakwanitse kuwerenga malembawo kapena kumutanthauzira mfumu. Onani mutuwo |