Danieli 5:5 - Buku Lopatulika5 Nthawi yomweyo zinabuka zala za dzanja la munthu, ndipo zinalemba pandunji pa choikaponyali, pomata pa khoma la chinyumba cha mfumu; ndipo mfumu inaona nsonga yake ya dzanja lidalembalo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Nthawi yomweyo zinabuka zala za dzanja la munthu, nizinalemba pandunji pa choikapo nyali, pomata pa khoma la chinyumba cha mfumu; ndipo mfumu inaona nsonga yake ya dzanja lidalembalo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mwadzidzidzi zala za dzanja la munthu zinaonekera ndi kulemba pa khoma, pafupi ndi choyikapo nyale mʼnyumba yaufumu. Mfumu inapenyetsetsa dzanjalo pamene limalemba. Onani mutuwo |