Danieli 3:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo amuna atatu awa, Sadrake, Mesaki, ndi Abedenego, anagwa pansi omangidwa m'kati mwa ng'anjo yotentha yamoto. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo amuna atatu awa, Sadrake, Mesaki, ndi Abedenego, anagwa pansi omangidwa m'kati mwa ng'anjo yotentha yamoto. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 ndipo anyamata atatuwa, ali chimangidwire, anagwera mʼngʼanjo ya moto. Onani mutuwo |