Danieli 2:33 - Buku Lopatulika33 miyendo yake yachitsulo, mapazi ake mwina chitsulo mwina dongo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 miyendo yake yachitsulo, mapazi ake mwina chitsulo mwina dongo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Miyendo yake inali yachitsulo, mapazi ake anali achitsulo chosakaniza ndi dongo. Onani mutuwo |