Danieli 2:20 - Buku Lopatulika20 Daniele anayankha, nati, Lilemekezedwe dzina la Mulungu kunthawi za nthawi, pakuti nzeru ndi mphamvu zili zake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Daniele anayankha, nati, Lilemekezedwe dzina la Mulungu kunthawi za nthawi, pakuti nzeru ndi mphamvu zili zake; Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 ndipo anati: “Litamandike dzina la Mulungu ku nthawi za nthawi; nzeru ndi mphamvu zonse ndi zake. Onani mutuwo |