Danieli 12:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo anati, Pita Daniele; pakuti mauwo atsekedwa, nakhomeredwa chizindikiro mpaka nthawi ya chitsiriziro. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo anati, Pita Daniele; pakuti mauwo atsekedwa, nakomeredwa chizindikiro mpaka nthawi ya chitsiriziro. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ndipo anandiyankha kuti, “Pita iwe Danieli, pakuti mawuwa ndi osungidwa ndi omatidwa kufikira nthawi ya chimaliziro. Onani mutuwo |