Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Danieli 11:9 - Buku Lopatulika

9 Ndipo adzalowa mu ufumu wa mfumu ya kumwera, koma adzabwera m'dziko lakelake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo adzalowa m'ufumu wa mfumu ya kumwera, koma adzabwera m'dziko lakelake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Kenaka mfumu ya kumpoto idzathira nkhondo dziko la mfumu ya kummwera koma idzalephera ndi kubwerera kwawo.

Onani mutuwo Koperani




Danieli 11:9
6 Mawu Ofanana  

Ndi ana ake adzachita nkhondo, nadzamemeza makamu a nkhondo aakulu ochuluka, amene adzalowa, nadzasefukira, nadzapita; ndipo adzabwerera, nadzachita nkhondo mpaka linga lake.


Ndi mfumu ya kumwera idzawawidwa mtima, nidzatuluka kulimbana naye, ndiye mfumu ya kumpoto imene idzaonetsa unyinji waukulu; koma unyinjiwo udzaperekedwa m'dzanja lake.


Ndipo mfumu ya kumwera, ndiye wina wa akalonga ake, idzamposa mphamvu, nidzakhala nao ulamuliro; ulamuliro wake ndi ulamuliro waukulu.


ndi milungu yao yomwe, pamodzi ndi akalonga ao, ndi zipangizo zao zofunika zasiliva ndi golide adzazitenga kunka nazo ndende ku Ejipito; ndi zaka zake zidzaposa za mfumu ya kumpoto.


Galeta wa akavalo akuda atulukira kudziko la kumpoto; ndi oyerawo atulukira kuwatsata; ndi amawanga atulukira kudziko la kumwera.


Iwo adzachita nkhondo pa Mwanawankhosa, ndipo Mwanawankhosa adzawagonjetsa, chifukwa ali Mbuye wa ambuye, ndi Mfumu ya mafumu; ndipo adzawalakanso iwo akukhala naye, oitanidwa, ndi osankhika ndi okhulupirika.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa