Danieli 1:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Mulungu anamkometsera Daniele mtima wa mkulu wa adindo, amchitire chifundo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Mulungu anamkometsera Daniele mtima wa mkulu wa adindo, amchitire chifundo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ndipo Mulungu anafewetsa mtima wa ndunayo kuti amukomere mtima ndi kumuchitira chifundo Danieli, Onani mutuwo |