Chivumbulutso 4:3 - Buku Lopatulika3 ndipo maonekedwe a Iye wokhalapo anafanana ndi mwala wa jaspi, ndi sardiyo; ndipo panali utawaleza wozinga mpando wachifumu, maonekedwe ake ngati smaragido. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 ndipo maonekedwe a Iye wokhalapo anafanana ndi mwala wa jaspi, ndi sardiyo; ndipo panali utawaleza wozinga mpando wachifumu, maonekedwe ake ngati smaragido. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Amene adaakhala pampandoyo, maonekedwe ake anali oŵala ngati miyala yoyera ndi yofiira, yonyezimira. Pozungulira mpando wachifumuwo panali utawaleza, maonekedwe ake ngati mwala woŵala, wobiriŵira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ndipo amene anakhalapoyo anali wa maonekedwe ngati miyala ya jasipa ndi sardiyo. Utawaleza wooneka ngati simaragido unazinga mpando waufumuwo. Onani mutuwo |