Amosi 4:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo mudzatulukira popasuka linga, yense m'tsogolo mwake, ndi kutayika ku Harimoni, ati Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo mudzatulukira popasuka linga, yense m'tsogolo mwake, ndi kutayika ku Harimoni, ati Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mudzatulukira m'ming'alu ya malinga, aliyense payekhapayekha ndipo adzakutayani ku phiri la Halimoni.” Akuterotu Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mudzatulukira mʼmingʼalu ya pa khoma aliyense payekhapayekha, ndipo mudzatayidwa ku Harimoni,” akutero Yehova. Onani mutuwo |