Amosi 4:12 - Buku Lopatulika12 Chifukwa chake ndidzatero nawe, Israele; popeza ndidzakuchitira ichi, dzikonzeretu kukomana ndi Mulungu wako, Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Chifukwa chake ndidzatero nawe, Israele; popeza ndidzakuchitira ichi, dzikonzeretu kukomana ndi Mulungu wako, Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 “Tsono inu Aisraele ndidzakuteroni. Ndipo chifukwa choti ndidzakuchitani zimenezi, inu Aisraele, konzekani kuti mukumane ndi Mulungu wanu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 “Choncho izi ndi zimene ndidzakuchitire iwe Israeli, chifukwa ndidzakuchitira zimenezi, konzekera kukumana ndi Mulungu wako, iwe Israeli.” Onani mutuwo |